Salimo 125:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Yehova, chitirani zabwino anthu abwino,+Anthu owongoka mtima.+ Miyambo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti owongoka mtima ndi amene adzakhale m’dziko lapansi,+ ndipo opanda cholakwa ndi amene adzatsalemo.+
21 Pakuti owongoka mtima ndi amene adzakhale m’dziko lapansi,+ ndipo opanda cholakwa ndi amene adzatsalemo.+