Salimo 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pali mtsinje womwe nthambi zake zimachititsa anthu a mumzinda wa Mulungu kukondwera,+Chihema chachikulu chopatulika koposa cha Wam’mwambamwamba.+ Salimo 87:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwe mzinda wa Mulungu woona, anthu akunena za ulemerero wako.+ [Seʹlah.]
4 Pali mtsinje womwe nthambi zake zimachititsa anthu a mumzinda wa Mulungu kukondwera,+Chihema chachikulu chopatulika koposa cha Wam’mwambamwamba.+