Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Patapita nthawi, Kaini anagona ndi mkazi wake+ ndipo mkaziyo anatenga pakati n’kubereka Inoki. Ndiyeno Kaini anayamba kumanga mzinda umene anautcha dzina la mwana wake lakuti Inoki.+

  • 1 Samueli 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako Samueli anadzuka m’mawa kwambiri kuti akaonane ndi Sauli. Koma uthenga unam’peza Samueli wonena kuti: “Sauli anabwera ku Karimeli,+ ndipotu waimika chipilala+ cha chikumbutso chake, kenako watembenuka ndipo wapita ku Giligala.”

  • 2 Samueli 18:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tsopano Abisalomu akali moyo anadzimangira chipilala.+ Chipilala chimenechi chili m’Chigwa cha Mfumu,+ pakuti iye anati: “Ine ndilibe mwana wamwamuna woti asunge dzina langa monga chikumbukiro.”+ Choncho chipilala chimenecho anachitcha dzina lake+ ndipo chikudziwikabe ndi dzina lakuti Chipilala cha Abisalomu kufikira lero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena