Genesis 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Mulungu anati: “Dziko lapansi+ likhale ndi zamoyo monga mwa mitundu yake, nyama zoweta,+ nyama zokwawa,*+ komanso nyama zakutchire+ monga mwa mitundu yake.” Ndipo zinaterodi. 1 Mbiri 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ndine ndani ine,+ ndipo anthu anga ndani kuti tithe kupereka nsembe zaufulu ngati zimenezi?+ Pakuti chilichonse n’chochokera kwa inu,+ ndipo tapereka kwa inu zochokera m’dzanja lanu. Yobu 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndinapanga mvuu* ndipo ndinapanganso iweyo.Iyo imadya udzu wobiriwira+ ngati ng’ombe yamphongo.
24 Tsopano Mulungu anati: “Dziko lapansi+ likhale ndi zamoyo monga mwa mitundu yake, nyama zoweta,+ nyama zokwawa,*+ komanso nyama zakutchire+ monga mwa mitundu yake.” Ndipo zinaterodi.
14 “Ndine ndani ine,+ ndipo anthu anga ndani kuti tithe kupereka nsembe zaufulu ngati zimenezi?+ Pakuti chilichonse n’chochokera kwa inu,+ ndipo tapereka kwa inu zochokera m’dzanja lanu.
15 Ine ndinapanga mvuu* ndipo ndinapanganso iweyo.Iyo imadya udzu wobiriwira+ ngati ng’ombe yamphongo.