Machitidwe 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno poona munthu wochiritsidwa uja ataimirira nawo limodzi,+ analibe chonena kuti awatsutse.+ Machitidwe 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwo sanathe kulimbana ndi nzeru+ zimene anasonyeza komanso mzimu woyera umene unali kumutsogolera pamene anali kulankhula.+
10 Koma iwo sanathe kulimbana ndi nzeru+ zimene anasonyeza komanso mzimu woyera umene unali kumutsogolera pamene anali kulankhula.+