Yeremiya 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wakutchulani dzina+ lakuti, ‘Mtengo waukulu wa maolivi wa masamba ambiri obiriwira, wokongola, wobala zipatso komanso wooneka bwino.’ Koma pali phokoso lamphamvu ndipo mtengowo auyatsa moto, komanso adani athyola nthambi zake.+ Hoseya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthambi zake zidzaphukira ndipo adzakhala ndi ulemerero ngati mtengo wa maolivi.+ Fungo lake lonunkhira lidzakhala ngati mtengo wa ku Lebanoni.
16 Yehova wakutchulani dzina+ lakuti, ‘Mtengo waukulu wa maolivi wa masamba ambiri obiriwira, wokongola, wobala zipatso komanso wooneka bwino.’ Koma pali phokoso lamphamvu ndipo mtengowo auyatsa moto, komanso adani athyola nthambi zake.+
6 Nthambi zake zidzaphukira ndipo adzakhala ndi ulemerero ngati mtengo wa maolivi.+ Fungo lake lonunkhira lidzakhala ngati mtengo wa ku Lebanoni.