Salimo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atumize thandizo kuchokera kumalo oyera.+Akuchirikizeni ali ku Ziyoni.+ Yesaya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+
6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+