Salimo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zingwe za imfa zinandikulunga,+Chikhamu cha anthu opanda pake chinali kundiopseza.+ Salimo 116:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zingwe za imfa zinandizungulira+Ndipo ndinasautsika ngati kuti ndili m’Manda.+Ndinapitiriza kusautsika ndi kukhala wachisoni,+ Yesaya 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndinati: “Pakatikati pa masiku anga ndidzalowa pazipata+ za Manda.Ndidzamanidwa zaka zanga zotsala.”+
3 Zingwe za imfa zinandizungulira+Ndipo ndinasautsika ngati kuti ndili m’Manda.+Ndinapitiriza kusautsika ndi kukhala wachisoni,+
10 Ine ndinati: “Pakatikati pa masiku anga ndidzalowa pazipata+ za Manda.Ndidzamanidwa zaka zanga zotsala.”+