-
Oweruza 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Pamenepo Adoni-bezeki anathawa, ndipo anam’thamangitsa ndi kum’gwira. Atam’gwira, anam’dula zala zamanthu za m’manja ndi zala zazikulu za kumapazi.
-