2 Samueli 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo Davide anadzipangira dzina atabwerako kumene anapha Aedomu 18,000+ m’chigwa cha Mchere.+ 1 Mbiri 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anapha Hadadezeri+ mfumu ya Zoba+ ku Hamati,+ pamene Hadadezeriyo anali kupita kumtsinje wa Firate+ kukakhazikitsa ulamuliro wake kumeneko.
3 Davide anapha Hadadezeri+ mfumu ya Zoba+ ku Hamati,+ pamene Hadadezeriyo anali kupita kumtsinje wa Firate+ kukakhazikitsa ulamuliro wake kumeneko.