Salimo 106:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno madzi anamiza adani awo,+Moti panalibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+