Deuteronomo 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndileke ndiwawononge+ ndi kufafaniza dzina lawo pansi pa thambo,+ ndipo ndikupange mtundu wamphamvu ndi waukulu kwambiri kuposa iwo.’+ Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+
14 Ndileke ndiwawononge+ ndi kufafaniza dzina lawo pansi pa thambo,+ ndipo ndikupange mtundu wamphamvu ndi waukulu kwambiri kuposa iwo.’+