Yesaya 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Taonani! Mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi lochokera mumtsuko, ndipo kwa iye ili ngati fumbi pasikelo.+ Iyetu amanyamula zilumba+ ngati kuti ndi fumbi.
15 Taonani! Mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi lochokera mumtsuko, ndipo kwa iye ili ngati fumbi pasikelo.+ Iyetu amanyamula zilumba+ ngati kuti ndi fumbi.