Salimo 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+ Salimo 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+
4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+
14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+