Salimo 48:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anaona ndipo anadabwa.Anasokonezeka, moti anathawa mopanikizika kwambiri.+ Salimo 66:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muuzeni Mulungu kuti: “Ntchito zanu ndi zochititsadi mantha!+Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zanu, adani anu adzabwera kwa inu mogonjera.+
3 Muuzeni Mulungu kuti: “Ntchito zanu ndi zochititsadi mantha!+Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zanu, adani anu adzabwera kwa inu mogonjera.+