Salimo 138:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mafumu onse a padziko lapansi adzakutamandani, inu Yehova,+Pakuti adzakhala atamva mawu a pakamwa panu. Salimo 142:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nditulutseni mundende ya mdima+Kuti nditamande dzina lanu.+Chititsani kuti anthu olungama asonkhane ndi kundizungulira,+Chifukwa mumandichitira zabwino.+
4 Mafumu onse a padziko lapansi adzakutamandani, inu Yehova,+Pakuti adzakhala atamva mawu a pakamwa panu.
7 Nditulutseni mundende ya mdima+Kuti nditamande dzina lanu.+Chititsani kuti anthu olungama asonkhane ndi kundizungulira,+Chifukwa mumandichitira zabwino.+