Salimo 44:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tidzayamika Mulungu nthawi zonse,+Tidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale.+ [Seʹlah.]