Oweruza 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri anasungunuka ndi kuyenda ngati madzi, kuchoka pamaso pa Yehova,+Sinai+ uyu anayenda ngati madzi kuchoka pamaso pa Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.+
5 Mapiri anasungunuka ndi kuyenda ngati madzi, kuchoka pamaso pa Yehova,+Sinai+ uyu anayenda ngati madzi kuchoka pamaso pa Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.+