Yeremiya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzapita kwa akuluakulu ndi kulankhula nawo,+ pakuti mosakayikira aganizira njira ya Yehova ndi chilamulo cha Mulungu wawo.+ Ndithudi onsewo athyola goli la Mulungu ndipo mosakayikira adula zomangira za Mulungu.”+
5 Ndidzapita kwa akuluakulu ndi kulankhula nawo,+ pakuti mosakayikira aganizira njira ya Yehova ndi chilamulo cha Mulungu wawo.+ Ndithudi onsewo athyola goli la Mulungu ndipo mosakayikira adula zomangira za Mulungu.”+