Ekisodo 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi ana a Isiraeli anadutsa pakati pa nyanja, panthaka youma,+ madziwo ataima ngati khoma* kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+ Yesaya 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unasandutsa pansi pa nyanja kukhala njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+
22 Patapita nthawi ana a Isiraeli anadutsa pakati pa nyanja, panthaka youma,+ madziwo ataima ngati khoma* kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+
10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unasandutsa pansi pa nyanja kukhala njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+