Salimo 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Phazi langa lidzaimadi pamalo athyathyathya.+Pamsonkhano, ndidzatamanda Yehova.+ Salimo 107:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Amukweze mumpingo wa anthu,+Ndipo amutamande m’bwalo la anthu achikulire.+