Ezekieli 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Phokoso la mapiko a akerubiwo+ linali kumveka mpaka kubwalo lakunja. Phokosolo linali kumveka ngati kulankhula kwa Mulungu Wamphamvuyonse.+
5 Phokoso la mapiko a akerubiwo+ linali kumveka mpaka kubwalo lakunja. Phokosolo linali kumveka ngati kulankhula kwa Mulungu Wamphamvuyonse.+