Salimo 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ananditulutsanso m’dzenje la madzi a mkokomo,+Ananditulutsa m’chithaphwi cha matope.+Kenako anapondetsa phazi langa pathanthwe.+Anandiyendetsa panthaka yolimba.+ Salimo 88:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwandiika m’dzenje lakuya kwambiri,M’malo a mdima, m’phompho lalikulu.+ Yeremiya 38:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero iwo anagwira Yeremiya ndi kumuponya m’chitsime cha Malikiya+ mwana wa mfumu, chimene chinali m’Bwalo la Alonda.+ Iwo anatsitsira Yeremiya m’chitsimemo ndi zingwe. M’chitsimemo munalibe madzi koma munali matope, ndipo Yeremiya anayamba kumira m’matopemo.+
2 Iye ananditulutsanso m’dzenje la madzi a mkokomo,+Ananditulutsa m’chithaphwi cha matope.+Kenako anapondetsa phazi langa pathanthwe.+Anandiyendetsa panthaka yolimba.+
6 Chotero iwo anagwira Yeremiya ndi kumuponya m’chitsime cha Malikiya+ mwana wa mfumu, chimene chinali m’Bwalo la Alonda.+ Iwo anatsitsira Yeremiya m’chitsimemo ndi zingwe. M’chitsimemo munalibe madzi koma munali matope, ndipo Yeremiya anayamba kumira m’matopemo.+