Salimo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Mulungu wanga, chikhulupiriro changa chili mwa inu.+Musalole kuti ndichite manyazi.Adani anga asakondwere chifukwa cha masautso anga.+ Salimo 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndathawira kwa inu Yehova.+Musalole kuti ndichite manyazi.+Ndipulumutseni chifukwa cha chilungamo chanu.+
2 Inu Mulungu wanga, chikhulupiriro changa chili mwa inu.+Musalole kuti ndichite manyazi.Adani anga asakondwere chifukwa cha masautso anga.+
31 Ndathawira kwa inu Yehova.+Musalole kuti ndichite manyazi.+Ndipulumutseni chifukwa cha chilungamo chanu.+