Salimo 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ananditulutsanso m’dzenje la madzi a mkokomo,+Ananditulutsa m’chithaphwi cha matope.+Kenako anapondetsa phazi langa pathanthwe.+Anandiyendetsa panthaka yolimba.+ Salimo 86:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+
2 Iye ananditulutsanso m’dzenje la madzi a mkokomo,+Ananditulutsa m’chithaphwi cha matope.+Kenako anapondetsa phazi langa pathanthwe.+Anandiyendetsa panthaka yolimba.+
13 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene mwandisonyeza ndi kwakukulu,+Ndipo mwapulumutsa moyo wanga ku Manda, kumalo apansi penipeni.+