1 Mbiri 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akupatse nzeru ndi kuzindikira.+ Akupatsenso lamulo lotsogolera Isiraeli, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.+ 1 Mbiri 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mupatse Solomo mwana wanga mtima wathunthu+ kuti asunge malamulo anu,+ maumboni* anu,+ ndi kuti achite zonse. Ndiponso kuti amange chinyumba chachikulu+ chimene ndakonzeratu zipangizo zake.”+
12 Yehova akupatse nzeru ndi kuzindikira.+ Akupatsenso lamulo lotsogolera Isiraeli, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.+
19 Mupatse Solomo mwana wanga mtima wathunthu+ kuti asunge malamulo anu,+ maumboni* anu,+ ndi kuti achite zonse. Ndiponso kuti amange chinyumba chachikulu+ chimene ndakonzeratu zipangizo zake.”+