Salimo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu inu, musakhale ngati hatchi kapena nyulu* yosazindikira,+Imene munthu amachita kuimanga chingwe chapakamwa ndi chapamutu kuti athetse kupulupudza kwake,+Ndi kuti aiyandikire.”+
9 Anthu inu, musakhale ngati hatchi kapena nyulu* yosazindikira,+Imene munthu amachita kuimanga chingwe chapakamwa ndi chapamutu kuti athetse kupulupudza kwake,+Ndi kuti aiyandikire.”+