Yobu 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Otemberera masiku alitemberere tsikulo,Iwo amene ali okonzeka kudzutsa ng’ona.*+ Yobu 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Kodi ungawedze ng’ona*+ ndi mbedza?Kapena ungamange lilime lake ndi chingwe? Salimo 104:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zombo zimayenda mmenemo.+Ndipo Leviyatani*+ munam’panga kuti azisewera mmenemo.+