4 Nthawi yomweyo Yefita anasonkhanitsa amuna onse a ku Giliyadi+ n’kumenyana ndi anthu a mu Efuraimu. Choncho amuna a ku Giliyadi anakantha Efuraimu, pakuti anati: “Ngakhale kuti inu anthu a mu Giliyadi mukukhala m’dera la Efuraimu ndi la Manase, kwenikweni ndinu gulu la anthu othawa ku Efuraimu.”