Salimo 106:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mofulumira anaiwala ntchito zake,+Iwo sanayembekezere malangizo ake.+ Salimo 106:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amene anachita zodabwitsa m’dziko la Hamu,+Amene anachita zochititsa mantha pa Nyanja Yofiira.+