Numeri 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+ Salimo 78:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma iwo anapitiriza kumuchimwira+Mwa kupandukira Wam’mwambamwamba m’dera lopanda madzi.+
11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+