Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mpongozi wake, mkazi wa Pinihasi, anali ndi pakati moti anali pafupi kubereka. Ndiyeno anamva kuti likasa la Mulungu woona lalandidwa ndipo apongozi ake ndi mwamuna wake afa. Zitatero, anawerama n’kuyamba kubereka, chifukwa zowawa za pobereka zinam’fikira mwadzidzidzi.+

  • Yobu 27:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Opulumuka ake adzaikidwa m’manda pa nthawi ya mliri wakupha,

      Ndipo akazi awo amasiye sadzalira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena