Amosi 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yesetsani kuyandikira kwa Yehova, inu a m’nyumba ya Yosefe,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndiponso kuti Mulungu asakuyakireni ngati moto.+ Chitani zimenezi kuti motowo usakunyeketseni chifukwa ku Beteli sikungapezeke munthu wouzimitsa.+
6 Yesetsani kuyandikira kwa Yehova, inu a m’nyumba ya Yosefe,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndiponso kuti Mulungu asakuyakireni ngati moto.+ Chitani zimenezi kuti motowo usakunyeketseni chifukwa ku Beteli sikungapezeke munthu wouzimitsa.+