Salimo 114:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 114 Pamene Isiraeli anatuluka mu Iguputo,+Pamene nyumba ya Yakobo inatuluka pakati pa anthu olankhula zosamveka,+
114 Pamene Isiraeli anatuluka mu Iguputo,+Pamene nyumba ya Yakobo inatuluka pakati pa anthu olankhula zosamveka,+