1 Mbiri 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’masiku a Sauli, iwo anachita nkhondo ndi Ahagara+ n’kuwagonjetsa. Kenako anayamba kukhala m’mahema awo m’dera lonse lakum’mawa kwa Giliyadi.
10 M’masiku a Sauli, iwo anachita nkhondo ndi Ahagara+ n’kuwagonjetsa. Kenako anayamba kukhala m’mahema awo m’dera lonse lakum’mawa kwa Giliyadi.