Salimo 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndaiwalidwa ngati munthu wakufa amene anthu sakumukumbukiranso.+Ndakhala ngati chiwiya chosweka.+