Salimo 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Madzi akuya akufuulira madzi akuya,Kudzera mu mkokomo wa madzi otumphuka.Mafunde anu onse amphamvu,+Andimiza.+
7 Madzi akuya akufuulira madzi akuya,Kudzera mu mkokomo wa madzi otumphuka.Mafunde anu onse amphamvu,+Andimiza.+