Yobu 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Manda ndi ovundukuka pamaso pake,+Ndipo malo a chiwonongeko n’ngosavundikira. Mlaliki 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zonse zimapita kumalo amodzi.+ Zonse zinachokera kufumbi+ ndipo zonse zimabwerera kufumbi.+