Salimo 86:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikukutamandani inu Yehova Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse,+Ndipo ndidzalemekeza dzina lanu mpaka kalekale, Salimo 106:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 106 Tamandani Ya, anthu inu!+Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
12 Ndikukutamandani inu Yehova Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse,+Ndipo ndidzalemekeza dzina lanu mpaka kalekale, Salimo 106:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 106 Tamandani Ya, anthu inu!+Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
106 Tamandani Ya, anthu inu!+Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+