Yobu 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anatambasula kumpoto pamwamba pa malo opanda kanthu,+Ndipo anakoloweka dziko lapansi m’malere.