Salimo 100:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lowani pazipata zake ndi mawu oyamikira,+Lowani m’mabwalo ake ndi mawu otamanda.+Muyamikeni, tamandani dzina lake.+ Salimo 135:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu amene mukuimirira m’nyumba ya Yehova,+M’mabwalo a nyumba ya Mulungu wathu.+
4 Lowani pazipata zake ndi mawu oyamikira,+Lowani m’mabwalo ake ndi mawu otamanda.+Muyamikeni, tamandani dzina lake.+