1 Mbiri 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Njenjemerani ndi mantha* pamaso pake, inu anthu nonse okhala padziko lapansi!Ndiponso dziko lapansi ndi lokhazikika,Silidzagwedezeka ku nthawi zonse.+ Salimo 114:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha Ambuye, chita mantha aakulu dziko lapansi iwe,+Chita mantha aakulu chifukwa cha Mulungu wa Yakobo,
30 Njenjemerani ndi mantha* pamaso pake, inu anthu nonse okhala padziko lapansi!Ndiponso dziko lapansi ndi lokhazikika,Silidzagwedezeka ku nthawi zonse.+
7 Chifukwa cha Ambuye, chita mantha aakulu dziko lapansi iwe,+Chita mantha aakulu chifukwa cha Mulungu wa Yakobo,