Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Choncho anthuwo anaimabe patali pomwepo, koma Mose anayandikira mtambo wakuda uja kumene kunali Mulungu woona.+

  • 1 Mafumu 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa nthawi imeneyo Solomo anati: “Yehova anati adzakhala mu mdima wandiweyani.+

  • Salimo 18:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+

      Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,

      Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena