2 Mbiri 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inuyo mupite nokha ndipo limbani mtima kukamenya nkhondo.+ Mulungu woona angakuchititseni kugonja kwa adani anu, chifukwa Mulungu ali ndi mphamvu zomuthandiza+ munthu kapena zom’chititsa kugonja.”+
8 Inuyo mupite nokha ndipo limbani mtima kukamenya nkhondo.+ Mulungu woona angakuchititseni kugonja kwa adani anu, chifukwa Mulungu ali ndi mphamvu zomuthandiza+ munthu kapena zom’chititsa kugonja.”+