Yobu 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mphepo ya kum’mawa idzamunyamula n’kumusowetsa,+Ndipo idzamuchotsa pamalo pake.+ Yesaya 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Udzu wobiriwirawo wauma ndipo maluwawo afota+ chifukwa mpweya wa Yehova wauzirapo.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.+
7 Udzu wobiriwirawo wauma ndipo maluwawo afota+ chifukwa mpweya wa Yehova wauzirapo.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.+