Salimo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+ Amosi 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Yehova ndilo dzina+ la amene amamanga makwerero ake kumwamba+ ndi kumanganso nyumba pamwamba pa dziko lapansi limene analikhazikitsa,+ amene amaitana madzi akunyanja+ kuti awakhuthulire panthaka ya dziko lapansi.’+
11 Kenako anapanga mdima kukhala malo ake obisalamo,+Panali madzi akuda ndi mtambo wakuda,Zimene zinamuzungulira ngati msasa wake.+
6 “‘Yehova ndilo dzina+ la amene amamanga makwerero ake kumwamba+ ndi kumanganso nyumba pamwamba pa dziko lapansi limene analikhazikitsa,+ amene amaitana madzi akunyanja+ kuti awakhuthulire panthaka ya dziko lapansi.’+