Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 38:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Kodi mkango ungausakire nyama,

      Ndipo kodi ungakhutiritse mikango yamphamvu yanjala kwambiri,+

  • Yesaya 31:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Mkango umalira moopseza, ngakhale mkango wamphamvu,+ poteteza nyama imene wagwira. Abusa ambirimbiri akaitanidwa kuti adzauthamangitse, ngakhale umve mawu awo suchita mantha ndipo ngakhale azichita phokoso suopa. M’njira yomweyo, Yehova wa makamu adzatsika kuti achite nkhondo poteteza phiri la Ziyoni ndiponso poteteza phiri lake laling’ono.+

  • Amosi 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi mkango umabangula m’nkhalango usanagwire nyama?+ Kodi mkango wamphamvu umalira m’malo ake obisalamo usanagwire kalikonse?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena