Salimo 102:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova adzamangadi Ziyoni.+Iye ayenera kuonekera mu ulemerero wake.+ Aroma 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Chifukwa zinthu zonse zimachokera kwa iye ndipo iye ndi amene anazipanga ndiponso ndi zake.+ Ulemerero ukhale wake kwamuyaya.+ Ame. Agalatiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ulemu ukhale kwa Mulunguyo mpaka muyaya.+ Ame.
36 Chifukwa zinthu zonse zimachokera kwa iye ndipo iye ndi amene anazipanga ndiponso ndi zake.+ Ulemerero ukhale wake kwamuyaya.+ Ame.