Salimo 99:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu anapitiriza kulankhula nawo mumtambo woima njo ngati chipilala.+Iwo anasunga zikumbutso zake ndi malangizo amene anawapatsa.+
7 Mulungu anapitiriza kulankhula nawo mumtambo woima njo ngati chipilala.+Iwo anasunga zikumbutso zake ndi malangizo amene anawapatsa.+