Ekisodo 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anachitadi zomwezo. Choncho Aroni anatambasula dzanja lake ndi kumenya fumbi lapansi ndi ndodo yake, ndipo ntchentchezo zinayamba kuluma anthu ndi nyama zomwe. Fumbi lonse la m’dziko la Iguputo linasanduka ntchentche zoluma.+
17 Iwo anachitadi zomwezo. Choncho Aroni anatambasula dzanja lake ndi kumenya fumbi lapansi ndi ndodo yake, ndipo ntchentchezo zinayamba kuluma anthu ndi nyama zomwe. Fumbi lonse la m’dziko la Iguputo linasanduka ntchentche zoluma.+